Zama ndi wamphamvu!
Jessy Sakala
Vusi Malindi
CiNyanja

M’ngono wanga amacedwa
kugona.
Ndimauka m’mamawa cifukwa
ndine wa ngwilo!
kugona.
Ndimauka m’mamawa cifukwa
ndine wa ngwilo!
Ndine ndimatsegulako kuti
dzuwa lilowe.
dzuwa lilowe.
‘‘Ndiwe nthanda yanga,’’ amatelo amai kundiwuza.
Ndimadzisamba ndekha matsiku
onse, sindifunanso thandidzo ai.
onse, sindifunanso thandidzo ai.
Sindimaganiza zakuti madzi
ndiyodzidzila, kapena sopo wa kamtambo
wocapila dzobvala.
ndiyodzidzila, kapena sopo wa kamtambo
wocapila dzobvala.
Amai amandikumbutsa kuti
“osayiwala kutsuka mano”.
Ndimawayanka kuti “ine
ai, sindingaiwale ai!”
“osayiwala kutsuka mano”.
Ndimawayanka kuti “ine
ai, sindingaiwale ai!”
Ndikamalidza kusamba, ndimapatsa
moni agogo amuna ndi alongo
awo atate anga.
Ndimawafunila tsiku labwino.
moni agogo amuna ndi alongo
awo atate anga.
Ndimawafunila tsiku labwino.
Ndipo ndimabvala ndekha.
‘‘Ndine wamkulu tsopano amama,’’ ndimawaudza.
‘‘Ndine wamkulu tsopano amama,’’ ndimawaudza.
Ndimanga mabatani komanso
nthambo za nsapato ndekha.
nthambo za nsapato ndekha.
Ndimayesetsa kuti mbale wanga adziwe nkhani zonse za kusukulu.
Ndimacita zonse zothekela
munjira mukalasi.
munjira mukalasi.
Ndimacita zabwino zonsezi
tsiku ndi tsiku.
Koma
ndimakondetsetsa kusowela
kwambili!
tsiku ndi tsiku.
Koma
ndimakondetsetsa kusowela
kwambili!
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Zama ndi wamphamvu!
Author - Michael Oguttu
Translation - Jessy Sakala
Illustration - Vusi Malindi
Language - CiNyanja
Level - First sentences
Translation - Jessy Sakala
Illustration - Vusi Malindi
Language - CiNyanja
Level - First sentences
© Text: Uganda Community Libraries Association (Ugcla) Artwork: African Storybook Initiative 2014
Creative Commons: Attribution 4.0
Source www.africanstorybook.org
Creative Commons: Attribution 4.0
Source www.africanstorybook.org

