Kuwerengera Nyama
Bether Mwale-Moyo and Moffat Moyo
Rob Owen

Njovu imodzi ikupita kukamwa madzi.
Nyamalikiti ziwiri zipita kukamwa madzi.
Njati zitatu zikupita kukamwa madzi pamodzi ndi mbalame zitatu.
Mphalapala zisanu ndi mnjiri zisanu ndi imodzi zikupita kukamwa madzi.
Mbidzi zisanu ndi ziwiri zikuthamangira ku madzi.
Acule asanu ndi atatu ndi nsomba zisanu ndi zinai zikusambira m'madzi.
Mkango umodzi ukubangula. Nawonso ukufuna kukamwa madzi.
Ndani amene amawop mkango?
Njovu imozi ikumwa manzi pamozi na mkango.
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Kuwerengera Nyama
Author - Clare Verbeek, Thembani Dladla and Zanele Buthelezi
Adaptation - Bether Mwale-Moyo and Moffat Moyo
Illustration - Rob Owen
Language - CiNyanja
Level - First sentences
© School of Education and Development (UKZN) and African Storybook Initiative 2007
Creative Commons: Attribution 4.0
Source www.africanstorybook.org
Original source http://cae.ukzn.ac.za/resources/seedbooks.aspx


