Mphwanga Waulesi
Clare Verbeek
Mlungisi Dlamini

Ndimadzuka
ndi kusonkha moto.

1

Ndimabwatutsa
madzi.

2

Ndimadula
nkhuni.

3

Ndimabvundula
madzi  yomwe ali pa moto.

4

Ndimapsyera
munyumba.

5

Ndimatsuka
mbale.

6

Chifukwa
nchyani ndimagwira ncthitomwaphanvu ine ndekha?

7

Pamene
mphyanga akonda kusewera chabe!

8
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Mphwanga Waulesi
Author - Clare Verbeek, Thembani Dladla, Zanele Buthelezi
Translation - Gridon Mwale
Illustration - Mlungisi Dlamini
Language - CiNyanja
Level - First words