Kuwelenga Nyama
Clare Verbeek
Rob Owen

Njovu imozi ipita kumwa manzi.

1

Nyamalikiti ziwili zipita kumwa manzi.

2

Njati zitatu na mbalame zinayi nazo zipita kumwa manzi.

3

Mphalapala zisanu na minjili isanu ndi umozi ziyenda kumanzi.

4

Mbizi zisanu ndi ziwili zitamangila ku manzi.

5

Acule asanu ndi atatu ndiponso nsomba zisanu ndi zinayi zinyaya mumanzi.

6

Nkalamu imozi yauluma. Nayonso ifuna kumwa manzi. Nindani aopa nkalamu?

7

Njovu imozi ikumwa manzi pamozi na nkalamu.

8
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Kuwelenga Nyama
Author - Clare Verbeek, Thembani Dladla, Zanele Buthelezi
Translation - Bether Mwale-Moyo, Moffat Moyo
Illustration - Rob Owen
Language - CiNyanja
Level - First words