Njere yaing'ono: Nkhani ya Wangari Maathai
Nicola Rijsdijk
Maya Marshak

M'mudzi wina wa tsinde la phiri la Kenya kum'mawa kwa Afirika, kudali mtsikana yemwe amagwila ntchito mminda ndi amaye ake.

Dzina la mtsikanayu lidali Wangari

1

Wangari amakonda kukhala panja.

Mmunda womwe amadzala chakudya chao anaswa mpanje

Adafesa tinjere munthakamo

2

Iye amakondetsetsa dzuwa likamalowa, pakuti madziwa kuti ndithawi yopita kunyumba.

Iye amayenda pa kanjira kakang'ono nawolokanso mitsinje pomwe amanka kunyumba

3

Wangari adali mwana ochenjera ndipo samakhumbitsitsi kupita ku sukulu.

Atafika dzaka zisanu ndi ziwiri, mchimwene wake adakopa makolo ake kuti akayambe school

4

5

6

Iye pophunzila zambiri amazindikilanso kuti akuwakonda kwambiri anthu a ku Krnya. Iye amafuna iwo adzikhala okondwa komanso omasuka nthawi zonse

Wangari akamaphunzila amakumbukila kwao ku Afirika

7

Atamaliza maphunzilo ake adabwelela ku Kenya.

Azimayi adalibe nkhuni zophikila chifukwa khalango yonse ija idakhala minda yolimamo mbeu zawo.

Umphawi koanso njala zidalikita anthu m'mudzimo

8

9

Pakupita kwa nthawi; mitengoyo idakula nakhala nkhalango, ndipo izi zidathandiza kubwezeletsedwa kwa mitsinje.

Uthenga wa Wangari ufalikila dera lonse la Afirika. Lero, zikwi zikwi za mitengo idadzalidwa nakula kuchokera ku mbeu za Wangari

10

Chifukwa cha ntchito yake yosalama za chilengedwe ndi anthu, Wangari adapaphana napeza mphoto ya maiko akunja yotchedwa Nobel Peace.

Mu chaka cha 2004, Wangari Maathai adali mzimayi wakuda kuchokera ku Afirika kupeza mphoto ya Nobel Peace komanso katswiri owona za chilengedwe

11

Wangari adamwalira mu chaka cha 2011, iye amakumbukilidwa nthawi zomwe pomwe taona ntengo wanthanzi.

Titha kupitiliza nthito yake podzala mitengo komanso kusamalila nkhalango zathu.

12
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Njere yaing'ono: Nkhani ya Wangari Maathai
Author - Nicola Rijsdijk
Translation - Peter Chamgwera
Illustration - Maya Marshak
Language - ChiChewa
Level - Longer paragraphs